31/08/2026
🇿🇦✈️ MAULENDO OPITA KU SOUTH AFRICA AYAMBANSO! 🇿🇦❤️
Kwa onse omwe akufuna kupita Ku south Africa koma akufuna transporter ndili okondwera kukudziwisani kuti ndayambilaso ulendo opita Ku south Africa nde Kwa omwe akufuna thandizo lililonse Kaya kuoda katundu kutumiza katundu Kaya mufuna kupita Ku south Africa
Ndiyankhuleni kuti mudziwe zambiri