03/06/2026
Akasi muli bwa? Ndakubweretseranitu chigayo cha mpunga Ndi nsinjiro ichi.Zonse mommo inde, mukafuna kukonola mpunga ndekut m***a kutero mpunga ochuluka 180kgs pa Ola pomwe ngati mugaya Kaya mtedza, chimanga, soya, nyemba, mapira Kaya mawere mugaya 250kgs pa Ola limodzi. Chigayochi sichifuna magetsina 3 phase ai omwewa apakhomowa (single phase) ndiwotheka. Taganizani kuika pa shop yanu uja uku mukugulitsa mbali inayi mukuwagaya za anthu ena, akasi kuiphulatu kuli pafupi. Nde mudziwa akasi, chigayochi chinali pa K2,300,000 koma panopa tangokhwefula ntengo kufika pa K2,050,000. Zabwinozi sizakuphonyeni akasi.
Tipezeni ku Lilongwe kwa Kaphiri moyang'anizana Ndi Simso oil kapena ku Area 2 moyang'anizana Ndi Breadtalk. Muthanso kuimba phone pa 0993176176 kapena 0993890007.