Chalaweh Kitchen

Directions

Chalaweh Kitchen Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Chalaweh Kitchen, Restaurant, Kauma Area 41 Lilongwe, Lilongwe.

kodi 2pin iyi nde itiyo iyi
12/10/2026

kodi 2pin iyi nde itiyo iyi

kodi makolo simuwamvetsa kukoma week imeneyi inu tapezani wanu red velvet cake pa mtengo wa ziii osaboola mthumba inu ta...
12/10/2026

kodi makolo simuwamvetsa kukoma week imeneyi inu tapezani wanu red velvet cake pa mtengo wa ziii osaboola mthumba inu tangoimbani phone number 0996877210
0888049829

kodi mother's day makolo mwakonzera chani  kodi kwanuko sitibwera ??
12/10/2026

kodi mother's day makolo mwakonzera chani kodi kwanuko sitibwera ??

mukasowa ku chalaweh kitchen kopanda ta ndi uku ku Arivan Business Consultancy  tatiyeni paja akuti agula ma T-SHIRT kom...
12/10/2026

mukasowa ku chalaweh kitchen kopanda ta ndi uku ku Arivan Business Consultancy tatiyeni paja akuti agula ma T-SHIRT komaso meal kwa top fan Kodi inuyo zabwino ai 😁

12/10/2026

Avuta ndi a Escom kwathu kuno week now no power 🤔🤔 2pin iweyo

akaka ndika Friday koma nanga mesa magetsi skutipanga chipongwe komabe kodi inuyo zabwino ai 😁mother day kodi simutiitan...
11/10/2026

akaka ndika Friday koma nanga mesa magetsi skutipanga chipongwe komabe

kodi inuyo zabwino ai 😁

mother day kodi simutiitana

osaiwala tili ndi Arivan Business Consultancy tiyeni tiwapange support

10/10/2026

lero Saturday kupephera kupange red velvet cake ya 200k koma Escom iweyo umuziwe yesu sure

10/10/2026

mmmmh 😂 Escom iyi nde iti kaya since Thursday mpaka lero osayakha ai zikomo

incase yakuphonyani inu tawapezani awa ndi akatundu tikutitu Arivan Business Consultancy  go konko
09/10/2026

incase yakuphonyani inu tawapezani awa ndi akatundu tikutitu Arivan Business Consultancy go konko

nde cholephelera kumupatsa ma customer komaso ma followers ndi chani tiyeni konko
09/10/2026

nde cholephelera kumupatsa ma customer komaso ma followers ndi chani tiyeni konko

Address

Kauma Area 41 Lilongwe
Lilongwe
MOBILERESTAURANT

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chalaweh Kitchen posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category